Ekisodo 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Motero amene anali kuwagwiritsa ntchito aja anali kuwakakamiza+ kugwira ntchito ponena kuti: “Muzimaliza ntchito yanu. Aliyense azimaliza ntchito yake tsiku lililonse, ngati mmene munali kuchitira pamene udzu unali kupezeka.”+
13 Motero amene anali kuwagwiritsa ntchito aja anali kuwakakamiza+ kugwira ntchito ponena kuti: “Muzimaliza ntchito yanu. Aliyense azimaliza ntchito yake tsiku lililonse, ngati mmene munali kuchitira pamene udzu unali kupezeka.”+