Ekisodo 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova wanena kuti:+ “Ndimenya madzi a mumtsinje wa Nailo+ ndi ndodo imene ili m’dzanja langa, ndipo madzi asanduka magazi.+ Zikatero udziwa kuti ine ndine Yehova.+
17 Yehova wanena kuti:+ “Ndimenya madzi a mumtsinje wa Nailo+ ndi ndodo imene ili m’dzanja langa, ndipo madzi asanduka magazi.+ Zikatero udziwa kuti ine ndine Yehova.+