Ekisodo 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Patapita nthawi, Farao anaitana Mose ndi Aroni ndi kuwauza kuti: “Chondererani Yehova+ kuti achotse achule pa ine ndi anthu anga, pakuti ndikufuna kulola anthu anu kuti apite kukapereka nsembe kwa Yehova.”+
8 Patapita nthawi, Farao anaitana Mose ndi Aroni ndi kuwauza kuti: “Chondererani Yehova+ kuti achotse achule pa ine ndi anthu anga, pakuti ndikufuna kulola anthu anu kuti apite kukapereka nsembe kwa Yehova.”+