Ekisodo 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Farao anatumiza atumiki ake kukaona, ndipo anapezadi kuti palibe chiweto ngakhale chimodzi cha Aisiraeli chimene chinafa. Ngakhale zinali choncho, Farao anaumitsabe mtima wake,+ osalola ana a Isiraeli kupita.
7 Pamenepo Farao anatumiza atumiki ake kukaona, ndipo anapezadi kuti palibe chiweto ngakhale chimodzi cha Aisiraeli chimene chinafa. Ngakhale zinali choncho, Farao anaumitsabe mtima wake,+ osalola ana a Isiraeli kupita.