Ekisodo 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma kudera la Goseni kokha, kumene kunali ana a Isiraeli, sikunagwe matalala.+