Ekisodo 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako ananyamuka ku Elimu,+ ndipo pa tsiku la 15 la mwezi wachiwiri atachoka m’dziko la Iguputo, khamu lonse la ana a Isiraeli linafika kuchipululu cha Sini,+ chimene chili pakati pa Elimu ndi Sinai.
16 Kenako ananyamuka ku Elimu,+ ndipo pa tsiku la 15 la mwezi wachiwiri atachoka m’dziko la Iguputo, khamu lonse la ana a Isiraeli linafika kuchipululu cha Sini,+ chimene chili pakati pa Elimu ndi Sinai.