Ekisodo 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa tsiku lachitatu akhale okonzeka, chifukwa pa tsiku lachitatulo Yehova adzatsikira paphiri la Sinai pamaso pa anthu onse.+
11 Pa tsiku lachitatu akhale okonzeka, chifukwa pa tsiku lachitatulo Yehova adzatsikira paphiri la Sinai pamaso pa anthu onse.+