-
Ekisodo 21:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Koma ngati ng’ombe inali ndi chizolowezi chogunda anthu ndipo mwiniwake anachenjezedwapo koma sanali kuiyang’anira, ndiyeno yapha mwamuna kapena mkazi, ng’ombeyo iziponyedwa miyala ndipo mwiniwakeyo aziphedwanso.
-