Ekisodo 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kaya ng’ombeyo inagunda mwana wamwamuna kapena mwana wamkazi, mwiniwake aziweruzidwa malinga ndi chigamulo chimenechi.+
31 Kaya ng’ombeyo inagunda mwana wamwamuna kapena mwana wamkazi, mwiniwake aziweruzidwa malinga ndi chigamulo chimenechi.+