Ekisodo 25:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipo pamalo anayi a choikapo nyalecho pakhale masamba ofunga duwa opangidwa ngati maluwa a mtengo wa amondi, ndipo masambawo atsatizane ndi mfundo ndi maluwa.+
34 Ndipo pamalo anayi a choikapo nyalecho pakhale masamba ofunga duwa opangidwa ngati maluwa a mtengo wa amondi, ndipo masambawo atsatizane ndi mfundo ndi maluwa.+