Ekisodo 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’litali mwake, nsalu iliyonse ikhale mikono 28, ndipo m’lifupi mwake ikhale mikono inayi. Nsalu zonse muyezo wake ukhale wofanana.+
2 M’litali mwake, nsalu iliyonse ikhale mikono 28, ndipo m’lifupi mwake ikhale mikono inayi. Nsalu zonse muyezo wake ukhale wofanana.+