Ekisodo 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Upangenso ngowe 50 zagolide ndi kulumikiza nsalu za chihema chopatulika zija ndi ngowezo kuti nsaluzo zikhale chinsalu chimodzi cha chihema.+
6 Upangenso ngowe 50 zagolide ndi kulumikiza nsalu za chihema chopatulika zija ndi ngowezo kuti nsaluzo zikhale chinsalu chimodzi cha chihema.+