Ekisodo 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’litali nsalu iliyonse ikhale mikono 30,+ ndipo m’lifupi nsalu iliyonse ikhale mikono inayi. Nsalu zonse 11 zija muyezo wake ukhale wofanana.
8 M’litali nsalu iliyonse ikhale mikono 30,+ ndipo m’lifupi nsalu iliyonse ikhale mikono inayi. Nsalu zonse 11 zija muyezo wake ukhale wofanana.