-
Ekisodo 26:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndipo m’litali mwa chinsalu chija, mkono umodzi kumbali iyi ndi mkono umodzinso kumbali inayo, zikhale zolendewera mpaka m’munsi m’mbali mwa chihema chopatulika, kuphimba chihemacho mbali iyi ndi mbali inayo.
-