Ekisodo 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ndi zitsulo zake 40 zasiliva zokhazikapo mafelemu. Zitsulo ziwiri zikhale pansi pa felemu limodzi la mano awiri, zitsulo zinanso ziwiri pansi pa felemu lina la mano awiri.+
21 ndi zitsulo zake 40 zasiliva zokhazikapo mafelemu. Zitsulo ziwiri zikhale pansi pa felemu limodzi la mano awiri, zitsulo zinanso ziwiri pansi pa felemu lina la mano awiri.+