Ekisodo 26:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Umange chihema chopatulikacho motsatira pulani imene ndakuonetsa m’phiri.+