16 “Pachipata cha bwalo pakhale nsalu yowomba m’litali mwake ikhale mikono 20, ya ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota, wabwino kwambiri.+ Pakhale nsanamira zinayi ndi zitsulo zinayi zokhazikapo nsanamirazo.+