Ekisodo 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Bwaloli m’litali mwake likhale mikono 100,+ m’lifupi mwake mikono 50, ndipo msinkhu wake mikono isanu. Nsalu zake zikhale za ulusi wopota, wabwino kwambiri, ndipo zitsulo zake zokhazikapo nsanamira zikhale zamkuwa.
18 Bwaloli m’litali mwake likhale mikono 100,+ m’lifupi mwake mikono 50, ndipo msinkhu wake mikono isanu. Nsalu zake zikhale za ulusi wopota, wabwino kwambiri, ndipo zitsulo zake zokhazikapo nsanamira zikhale zamkuwa.