Ekisodo 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ndiyeno ubweretse Aroni ndi ana ake pakhomo+ la chihema chokumanako, ndipo uwalamule kuti asambe ndi madzi.+
4 “Ndiyeno ubweretse Aroni ndi ana ake pakhomo+ la chihema chokumanako, ndipo uwalamule kuti asambe ndi madzi.+