Ekisodo 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno ng’ombeyo uiphe pamaso pa Yehova, pakhomo la chihema chokumanako.+