Ekisodo 29:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nkhosa yonseyo uitenthe paguwa lansembe. Imeneyo ndi nsembe yopsereza+ yoperekedwa kwa Yehova, fungo lokhazika mtima pansi.+ Ndiyo nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.
18 Nkhosa yonseyo uitenthe paguwa lansembe. Imeneyo ndi nsembe yopsereza+ yoperekedwa kwa Yehova, fungo lokhazika mtima pansi.+ Ndiyo nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.