Ekisodo 29:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 M’dengu la mikate yosafufumitsa limene lili pamaso pa Yehova utengemo mtanda wobulungira wa mkate, mkate wozungulira woboola pakati wothira mafuta ndi mkate wopyapyala.+
23 M’dengu la mikate yosafufumitsa limene lili pamaso pa Yehova utengemo mtanda wobulungira wa mkate, mkate wozungulira woboola pakati wothira mafuta ndi mkate wopyapyala.+