Ekisodo 29:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pa nkhosa yolongera Aroni ndi ana ake unsembe,+ upatule nganga+ ya nsembe yoweyula imene anaweyula, ndi mwendo wa gawo lopatulika umene anapereka.
27 Pa nkhosa yolongera Aroni ndi ana ake unsembe,+ upatule nganga+ ya nsembe yoweyula imene anaweyula, ndi mwendo wa gawo lopatulika umene anapereka.