Ekisodo 29:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Kenako utenge nkhosa yowalongera unsembe ndi kuwiritsa nyama yake m’malo oyera.+