Ekisodo 29:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Adye zinthu zimene aphimbira machimo kuti apatsidwe mphamvu ndi kuyeretsedwa.+ Koma munthu wamba asadye nawo, chifukwa ndi zinthu zopatulika.+
33 Adye zinthu zimene aphimbira machimo kuti apatsidwe mphamvu ndi kuyeretsedwa.+ Koma munthu wamba asadye nawo, chifukwa ndi zinthu zopatulika.+