Ekisodo 29:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Udzatenga masiku 7 poperekera guwa lansembelo nsembe yophimba machimo. Udzaliyeretse+ kuti likhale guwa lansembe loyera koposa.+ Aliyense wokhudza guwa lansembe azikhala woyera.+
37 Udzatenga masiku 7 poperekera guwa lansembelo nsembe yophimba machimo. Udzaliyeretse+ kuti likhale guwa lansembe loyera koposa.+ Aliyense wokhudza guwa lansembe azikhala woyera.+