Ekisodo 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Upange guwa lansembe la zofukiza.+ Ulipange ndi matabwa a mthethe.