Ekisodo 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Aziteronso akamayatsa nyalezo madzulo.* Zimenezi ndi zofukiza zoyenera kuperekedwa kwa Yehova nthawi zonse m’mibadwo yanu yonse. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:8 Nsanja ya Olonda,7/1/1996, tsa. 9
8 Aziteronso akamayatsa nyalezo madzulo.* Zimenezi ndi zofukiza zoyenera kuperekedwa kwa Yehova nthawi zonse m’mibadwo yanu yonse.