-
Ekisodo 34:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Pamenepo Mose anawaitana. Chotero Aroni ndi atsogoleri onse a khamu la Isiraeli anabwerera kwa iye, ndipo Mose anayamba kulankhula nawo.
-