Ekisodo 34:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndipo ana a Isiraeli anali kuona kuti nkhope ya Mose ikuwala.+ Choncho Mose anali kuphimbanso nkhope yake mpaka atabwerera kukalankhula ndi Mulungu.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:35 Nsanja ya Olonda,3/15/1990, tsa. 7
35 Ndipo ana a Isiraeli anali kuona kuti nkhope ya Mose ikuwala.+ Choncho Mose anali kuphimbanso nkhope yake mpaka atabwerera kukalankhula ndi Mulungu.+