Ekisodo 37:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako analikuta ndi golide woyenga bwino mkati ndi kunja komwe, ndipo anapanga mkombero wagolide kuzungulira Likasalo.+
2 Kenako analikuta ndi golide woyenga bwino mkati ndi kunja komwe, ndipo anapanga mkombero wagolide kuzungulira Likasalo.+