Levitiko 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Zimenezi mudzazipereka kwa Yehova monga nsembe ya zipatso zoyambirira,+ chotero simuyenera kuzibweretsa paguwa lansembe kuti zikhale nsembe yafungo lokhazika mtima pansi.
12 “‘Zimenezi mudzazipereka kwa Yehova monga nsembe ya zipatso zoyambirira,+ chotero simuyenera kuzibweretsa paguwa lansembe kuti zikhale nsembe yafungo lokhazika mtima pansi.