Levitiko 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo wansembe azitentha chikumbutso+ cha nsembeyo, kapena kuti, tirigu wotibula uja pang’ono ndi mafuta, pamodzi ndi lubani wake yense, kuti zikhale nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.
16 Ndipo wansembe azitentha chikumbutso+ cha nsembeyo, kapena kuti, tirigu wotibula uja pang’ono ndi mafuta, pamodzi ndi lubani wake yense, kuti zikhale nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.