Levitiko 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kumeneko akulu a khamu la Isiraeli aziika manja awo pamutu wa ng’ombeyo+ pamaso pa Yehova, ndipo aziipha pamaso pa Yehova.
15 Kumeneko akulu a khamu la Isiraeli aziika manja awo pamutu wa ng’ombeyo+ pamaso pa Yehova, ndipo aziipha pamaso pa Yehova.