Levitiko 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Azitenganso ng’ombe ndi kukaitentha kunja kwa msasa monga mmene anatenthera ng’ombe yoyamba ija.+ Imeneyi ndi nsembe yamachimo ya mpingo wonse.+
21 Azitenganso ng’ombe ndi kukaitentha kunja kwa msasa monga mmene anatenthera ng’ombe yoyamba ija.+ Imeneyi ndi nsembe yamachimo ya mpingo wonse.+