Levitiko 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno azivula zovalazo+ ndi kuvala zina. Akatero, azitenga phulusa losakanizika ndi mafutalo kupita nalo kumalo oyera, kunja kwa msasa.+
11 Ndiyeno azivula zovalazo+ ndi kuvala zina. Akatero, azitenga phulusa losakanizika ndi mafutalo kupita nalo kumalo oyera, kunja kwa msasa.+