Levitiko 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pophika, musaikemo chofufumitsa chilichonse.+ Ndaupereka monga gawo lawo kuchokera pansembe zanga zotentha ndi moto.+ Zimenezi n’zopatulika+ koposa mofanana ndi nsembe yamachimo ndi nsembe ya kupalamula.
17 Pophika, musaikemo chofufumitsa chilichonse.+ Ndaupereka monga gawo lawo kuchokera pansembe zanga zotentha ndi moto.+ Zimenezi n’zopatulika+ koposa mofanana ndi nsembe yamachimo ndi nsembe ya kupalamula.