Levitiko 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo pa zimenezi azipereka mtanda umodzi wa nsembe iliyonse kuti ikhale gawo lopatulika loperekedwa kwa Yehova.+ Mtandawo uzikhala wa wansembe+ amene wawaza magazi a nsembe zachiyanjanozo paguwa lansembe.
14 Ndipo pa zimenezi azipereka mtanda umodzi wa nsembe iliyonse kuti ikhale gawo lopatulika loperekedwa kwa Yehova.+ Mtandawo uzikhala wa wansembe+ amene wawaza magazi a nsembe zachiyanjanozo paguwa lansembe.