Levitiko 7:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mwana wa Aroni amene wapereka kwa Mulungu magazi a nsembe zachiyanjano ndiponso mafuta, azitenga mwendo wakumbuyo wa kudzanja lamanja monga gawo lake.+
33 Mwana wa Aroni amene wapereka kwa Mulungu magazi a nsembe zachiyanjano ndiponso mafuta, azitenga mwendo wakumbuyo wa kudzanja lamanja monga gawo lake.+