Levitiko 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Mose anatenga mafuta odzozera n’kudzoza chihema chopatulika+ ndi zonse zimene zinali mkati mwake, n’kuzipatula.
10 Ndiyeno Mose anatenga mafuta odzozera n’kudzoza chihema chopatulika+ ndi zonse zimene zinali mkati mwake, n’kuzipatula.