Levitiko 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anawaza ena mwa mafuta odzozerawo maulendo 7 paguwa lansembe+ ndi kudzoza guwa lansembelo, zipangizo zake zonse, beseni ndi choikapo chake, n’kuzipatula.
11 Anawaza ena mwa mafuta odzozerawo maulendo 7 paguwa lansembe+ ndi kudzoza guwa lansembelo, zipangizo zake zonse, beseni ndi choikapo chake, n’kuzipatula.