Levitiko 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mose anapha nkhosayo ndi kutengako magazi ake n’kuwapaka m’munsi pakhutu la kudzanja lamanja la Aroni, pachala chake chamanthu kudzanja lamanja, ndi pachala chake chachikulu cha kumwendo wa kudzanja lamanja.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:23 Nsanja ya Olonda,11/15/2014, ptsa. 9-10
23 Mose anapha nkhosayo ndi kutengako magazi ake n’kuwapaka m’munsi pakhutu la kudzanja lamanja la Aroni, pachala chake chamanthu kudzanja lamanja, ndi pachala chake chachikulu cha kumwendo wa kudzanja lamanja.+