Levitiko 8:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo anatenga mafuta a nkhosayo, mchira wa mafuta, mafuta onse okuta matumbo,+ mafuta a pachiwindi, impso ziwiri ndi mafuta ake ndi mwendo wakumbuyo wa kudzanja lamanja.+
25 Pamenepo anatenga mafuta a nkhosayo, mchira wa mafuta, mafuta onse okuta matumbo,+ mafuta a pachiwindi, impso ziwiri ndi mafuta ake ndi mwendo wakumbuyo wa kudzanja lamanja.+