Levitiko 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno Mose anazitenga m’manja mwawo n’kuzitentha paguwa lansembe pamwamba pa nsembe yopsereza.+ Zimenezi zinali nsembe yowalongera unsembe,+ yafungo lokhazika mtima pansi.+ Inali nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.+
28 Ndiyeno Mose anazitenga m’manja mwawo n’kuzitentha paguwa lansembe pamwamba pa nsembe yopsereza.+ Zimenezi zinali nsembe yowalongera unsembe,+ yafungo lokhazika mtima pansi.+ Inali nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.+