Levitiko 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma uza ana a Isiraeli kuti, ‘Tengani mbuzi yamphongo+ kuti ikhale nsembe yamachimo. Mutengenso mwana wa ng’ombe ndi nkhosa yaing’ono yamphongo,+ zonsezi zikhale za chaka chimodzi, zopanda chilema, kuti zikhale nsembe yopsereza.
3 Koma uza ana a Isiraeli kuti, ‘Tengani mbuzi yamphongo+ kuti ikhale nsembe yamachimo. Mutengenso mwana wa ng’ombe ndi nkhosa yaing’ono yamphongo,+ zonsezi zikhale za chaka chimodzi, zopanda chilema, kuti zikhale nsembe yopsereza.