Levitiko 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chimodzimodzinso kalulu,+ chifukwa amabzikula, koma ziboda zake n’zosagawanika. Akhale wodetsedwa kwa inu. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:6 Nsanja ya Olonda,5/15/1992, tsa. 4 Kukambitsirana, tsa. 57
6 Chimodzimodzinso kalulu,+ chifukwa amabzikula, koma ziboda zake n’zosagawanika. Akhale wodetsedwa kwa inu.