Levitiko 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndipo munthu wonyamula iliyonse ya nyama zimenezi itafa,+ azichapa zovala zake,+ ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo. Nyama zimenezi zikhale zodetsedwa kwa inu.
28 Ndipo munthu wonyamula iliyonse ya nyama zimenezi itafa,+ azichapa zovala zake,+ ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo. Nyama zimenezi zikhale zodetsedwa kwa inu.