Levitiko 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo wansembe azionanso munthuyo, ndipo ngati nkhanambo yake yafalikira pakhungu, wansembeyo azigamula kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Limenelo ndi khate.+
8 Pamenepo wansembe azionanso munthuyo, ndipo ngati nkhanambo yake yafalikira pakhungu, wansembeyo azigamula kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Limenelo ndi khate.+