-
Levitiko 13:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 pamenepo wansembe aziona chilondacho. Ngati cheya cha pamenepo chasanduka choyera ndipo chilondacho chikuoneka chozama kupitirira khungu, limenelo ndi khate. Labuka pachilonda, ndipo wansembe azigamula kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Imeneyo ndi nthenda ya khate.
-