-
Levitiko 13:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Koma ngati kutuwa kwa pachilondapo sikunasinthe, osafalikira pakhungu, ndipo kwayamba kuzimiririka, kumeneko ndi kutupa kwa chilonda. Wansembe azigamula kuti munthuyo ndi woyera chifukwa kumeneko ndi kutukusira kwa chilonda.
-